Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

c Mfundo imodzi imene inachititsa kuti machenjezo ngati amenewa akhale opanda mphamvu inali yakuti machenjezowa kwenikweni ankapita kwa kagulu ka nkhosa ka 144,000. M’mutu 5 tidzaona kuti chisanafike chaka cha 1935, anthu ankakhulupirira kuti “khamu lalikulu” lofotokozedwa pa Chivumbulutso 7:9, 10, lidzapangidwa ndi anthu ambirimbiri a m’matchalitchi amene amati ndi achikhristu. Gulu limeneli lidzakhala gulu lachiwiri limene lidzalandire mphoto yawo kumwamba chifukwa chogwirizana ndi Khristu ngakhale kuti adzachita zimenezi nthawi itatha kale.

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena