Mawu a M'munsi d Rute ndi mmodzi mwa akazi anayi amene Baibulo limatchula pa mzere wa makolo a Yesu. Wina ndi Rahabi, yemwe anali mayi ake a Boazi. (Mat. 1:3, 5, 6, 16) Mofanana ndi Rute, nayenso Rahabi sanali Mwisiraeli.