Zimene Zili M’magaziniyi
M’MAGAZINIYI MULI
Nkhani yophunzira wiki ya May 4-10, 2026
2 Muziwonjezera ‘Luso Lanu Lophunzitsa’ mu Utumiki
Nkhani yophunzira wiki ya May 11-17, 2026
8 Muzidalira Wolamulira wa Chilengedwe Chonse
Nkhani yophunzira wiki ya May 18-24, 2026
14 Zimene Mungachite Kuti Mulimbane ndi Zosokoneza
Nkhani yophunzira wiki ya May 25-31, 2026
20 Muzikhala Ozindikira Kuti ‘Zinthu Zizikuyenderani Bwino’
Nkhani yophunzira wiki ya June 1-7, 2026
26 Tikhoza Kumasangalalabe Ngakhale Kuti Anthu Ena Amadana Nafe
32 Munthu Wotchulidwa M’Baibulo—Muzikhala Olimba Mtima Komanso Okhulupirika Ngati Benaya