Zimene Zili M’magaziniyi
M’MAGAZINIYI MULI
Nkhani Yophunzira 31: October 7-13, 2024
2 Zimene Yehova Wachita Kuti Atipulumutse ku Uchimo ndi Imfa
7 Mafunso Ochokera kwa Owerenga
Nkhani Yophunzira 32: October 14-20, 2024
8 Yehova Amafuna Kuti Anthu Onse Alape
Nkhani Yophunzira 33: October 21-27, 2024
14 Kodi Mpingo Ungatsanzire Bwanji Maganizo a Yehova pa Nkhani ya Anthu Ochimwa
Nkhani Yophunzira 34: October 28, 2024–November 3, 2024
20 Mmene Tingasonyezere Chikondi ndi Chifundo Wina Akachita Tchimo
Nkhani Yophunzira 35: November 4-10, 2024
26 Kodi Akulu Angathandize Bwanji Anthu Amene Achotsedwa Mumpingo