Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w23 August tsamba 1-32
  • Magazini Yophunzira

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Magazini Yophunzira
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
w23 August tsamba 1-32
Mneneri Danieli akuyang’ana kumwamba pomwe ali m’dzenje ndipo wazunguliridwa ndi mikango. Mngelo akuuluka pamwamba pake kuti amuteteze.

Magazini Yophunzira

AUGUST 2023

NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: OCTOBER 9–NOVEMBER 5, 2023

© 2023 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.

Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.

CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:

Yehova anadalitsa kukhulupirika kwa Danieli potumiza mngelo yemwe anatseka pakamwa pa mikango (Onani nkhani yophunzira 33, ndime 11)

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena