Nkhani Zimene Zatuluka Pa JW Library Komanso JW.ORG
KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?
Kupereka Chithandizo Padziko Lonse pa Nthawi ya Mliri
Zimene tachita popereka chithandizo pa nthawi ya mliri wa COVID-19 zadabwitsa a Mboni komanso amene si a Mboni.
NKHANI ZINA
Kodi Mayiko Angathe Kuyendetsa Chuma Mokomera Aliyense?
Anthu alephera kuyendetsa zachuma m’njira imene ingathandize aliyense. Baibulo limafotokoza zimene Mulungu adzachite kuti athetse vutoli.
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
Kodi Baibulo Lingandithandize Bwanji?—Gawo 1: Kuganizira Mozama Mfundo za M’Baibulo
Ngati mutapeza chikwama cha ndalama chomwe chikuoneka kuti ndi chakale, kodi simungakhale ndi chidwi kuti muone zimene zili mkatimo? Baibulo lili ngati chikwama choterocho. Mumapezeka mfundo zanzeru zomwe zingakuthandizeni.