Nkhani Zimene Zatuluka Pa JW Library Komanso JW.ORG
ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA
Tinasankha Kukhala Moyo Wosalira Zambiri
Madián ndi Marcela anaona kuti kumangokhalira kugula zinthu komanso kukhala ndi ngongole zazikulu kunkachititsa kuti azikhala ndi nkhawa, koma kuphunzitsa anthu za Mulungu kunawathandiza kuti azisangalala.
NKHANI ZINA
Kodi Baibulo Lingakuthandizeni Pakachitika Ngozi Zam’chilengedwe?
Malangizo a m’Baibulo angakuthandizeni pasanachitike ngozi zam’chilengedwe, pamene zikuchitika komanso pambuyo pake.
MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA
Zimene Makolo Ayenera Kudziwa Zokhudza Kutumiza Mwana Kumalo Osamalira Ana Masana
Makolo asanasankhe kutumiza mwana wawo kumalo osamalira ana, ayenera kuganizira ubwino ndi kuipa kwake. Mafunso amene ali munkhaniyi angawathandize kudziwa zimene zingakhale zothandiza kwa mwana wawo.