Nkhani Zimene Zatuluka Pa JW Library Komanso JW.ORG
KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?
Kuthandiza Anthu Amene Akhudzidwa ndi Ngozi Zadzidzidzi
M’chaka chautumiki cha 2020 abale athu ambiri anakhudzidwa ndi mliri komanso ngozi zam’chilengedwe. Kodi tinachita zotani powathandiza?
Pa JW Library, pitani pamene alemba kuti PUBLICATIONS > ARTICLE SERIES > HOW YOUR DONATIONS ARE USED.
Pa jw.org, pitani pamene alemba kuti LAIBULALE > NKHANI ZOSIYANASIYANA > KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?
MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA
Muzipeza Nthawi Yochitira Zinthu Limodzi
Mwamuna ndi mkazi wake angamalephere kulankhulana ngakhale ali limodzi. Kodi anthu okwatirana angatani kuti azichitira zinthu limodzi?
Pa JW Library, pitani pamene alemba kuti PUBLICATIONS > ARTICLE SERIES > HELP FOR THE FAMILY.
Pa jw.org, pitani pamene alemba kuti LAIBULALE > NKHANI ZOSIYANASIYANA > MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA.