Magazini Yophunzira
JANUARY 2021
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: MARCH 1–APRIL 4, 2021
© 2020 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
A khamu lalikulu avala mikanjo yoyera, anyamula nthambi za kanjedza m’manja mwawo ndipo aimirira pamaso pa mpando wachifumu wa ulemelero wa Mulungu komanso pamaso pa Mwanawankhosa (Onani nkhani yophunzira 3, ndime 7)