Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w20 January tsamba 1-32
  • Magazini Yophunzira

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Magazini Yophunzira
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2020
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2020
w20 January tsamba 1-32
Nsanja ya Olonda Yophunzira, Januar 2020.

Magazini Yophunzira

JANUARY 2020

NKHANI ZOPHUNZIRA: MARCH 2–APRIL 5, 2020

© 2019 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

LEMBA LA CHAKA CHA 2020:

“Pitani mukaphunzitse anthu . . . kuti akhale ophunzira anga. Muziwabatiza.”​—MAT. 28:19.

Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.

Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.

CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:

Yesu ataukitsidwa anakumana ndi atumwi komanso anthu ena ku Galileya ndipo anawauza kuti “pitani mukaphunzitse anthu . . . kuti akhale ophunzira anga” (Onani nkhani yophunzira 1, ndime 3-4)

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena