Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsamba 10
  • August 14-20

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • August 14-20
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 July tsamba 10

August 14-20

NEHEMIYA 8-9

  • Nyimbo Na. 110 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka Ndicho Malo Anu Achitetezo”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Ne 8:2, 8​—Ngati anthu omwe anasonkhana “akanatha kumvetsera ndi kuzindikira” pamene Chilamulo chinkawerengedwa, n’chifukwa chiyani Alevi ankafunika kuchifotokozera? (it-1 145 ¶2)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Ne 8:1-12 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 13)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Muitanireni ku misonkhano yathu, ndipo yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani? kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 11)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 11 mfundo 5 komanso Zimene Ena Amanena (th phunziro 8)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 132

  • “Zochita Zanu Zingathandize Banja Lanu Kukhala Losangalala”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 54

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 123 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena