Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 March tsamba 14
  • April 24-30

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 24-30
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 March tsamba 14

April 24-30

2 MBIRI 13-16

  • Nyimbo Na. 3 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Ndi pa Nthawi Iti Pamene Tiyenera Kudalira Yehova?”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mb 15:16​—Kodi tingatsanzire bwanji kulimba mtima kwa Asa? (w17.03 19 ¶7)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mb 14:1-15 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako mufotokozereni za webusaiti yathu ya jw.org, ndipo mugawireni khadi lodziwitsa anthu za webusaitiyi. (th phunziro 1)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Muuzeni kuti timaphunzira Baibulo ndi anthu ndipo musiyireni khadi lodziwitsa anthu za phunziro la Baibulo. (th phunziro 11)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 09 mfundo 7 ndi Zimene Ena Amanena (th phunziro 6)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 94

  • “Zosankha Zomwe Zimasonyeza Kuti Timadalira Yehova”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 44 mfundo 1-4 ndi mawu akumapeto 5

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 39 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena