Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 March tsamba 12
  • April 17-23

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 17-23
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 March tsamba 12

April 17-23

2 MBIRI 10-12

  • Nyimbo Na. 103 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzitsatira Malangizo Anzeru”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mb 11:15​—Kodi mawu akuti “ziwanda zooneka ngati mbuzi” angakhale akunena za chiyani? (it-1 966-967)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mb 10:1-15 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 12)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 6)

  • Nkhani: (5 min.) be 69 ¶4-5​—Mutu: Ophunzira Baibulo Akafunsa Malangizo, Muziwaphunzitsa Mmene Angawapezere. (th phunziro 20)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 79

  • “Mmene Tingagwiritsire Ntchito Mavidiyo Onena za Kuphunzira Baibulo”: (5 min.) Nkhani komanso vidiyo. Onerani vidiyo yakuti Sangalalani Pophunzira Baibulo.

  • Zofunika Pampingo: (10 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 43

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 121 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena