Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 March tsamba 4
  • March 13-19

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 13-19
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 March tsamba 4

March 13-19

1 MBIRI 27-29

  • Nyimbo Na. 133 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Malangizo Achikondi a Bambo Opita kwa Mwana Wake”: (10 min.))

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 1Mb 27:33​—N’chifukwa chiyani Husai ali chitsanzo chabwino cha bwenzi lokhulupirika? (w17.03 29 ¶6-7)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mb 27:1-15 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya Ulendo Wobwereza: Yesu​—Mt 20:28. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Pangani ulendo wobwereza kwa munthu amene anasonyeza chidwi ndipo analandira kapepala komuitanira ku Chikumbutso. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti N’chifukwa chiyani Yesu anafa?, kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 9)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Pangani ulendo wobwereza kwa munthu amene anasonyeza chidwi ndipo analandira kapepala komuitanira ku Chikumbutso. Yambitsani phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 6)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 4

  • Zofunika Pampingo: (5 min.)

  • Zimene Gulu Lathu Lachita: (10 min.) Onerani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya March.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 40

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 45 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena