Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsamba 13
  • February 20-26

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • February 20-26
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 January tsamba 13

February 20-26

1 MBIRI 17-19

  • Nyimbo Na. 110 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzikhalabe Wosangalala Ngakhale Pamene Zinthu Sizikuyenda Bwino”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 1Mb 17:16-18​—Mofanana ndi Davide, kodi tingakhale otsimikiza mtima za chiyani? (w20.02 12, bokosi)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mb 18:1-17 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi a Mboni za Yehova ndi Anthu Otani? kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 17)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 3)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 09 mfundo 4 (th phunziro 9)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 64

  • Lipoti la Chaka Chautumiki: (15 min.) Nkhani yokambirana. Pambuyo powerenga chilengezo chochokera ku ofesi ya nthambi chokhudza lipoti la chaka chautumiki, funsani omvera kuti afotokoze zinthu zabwino zomwe zili mu Lipoti la Chaka cha Utumiki cha 2022 la Mboni za Yehova Padziko Lonse. Funsani ofalitsa omwe munawasankhiratu kuti afotokoze zinthu zolimbikitsa zimene anakumana nazo mu utumiki chaka chathachi.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 38 mfundo 1-4

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 141 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena