Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsamba 12
  • February 13-19

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • February 13-19
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 January tsamba 12

February 13-19

1 MBIRI 13-16

  • Nyimbo Na. 123 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Zinthu Zimatiyendera Bwino Tikamatsatira Malangizo”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 1Mb 16:31​—N’chifukwa chiyani Alevi anaimba kuti: “Yehova wakhala mfumu!”? (w14 1/15 10 ¶14)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mb 13:1-14 (th phunziro 11)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 18)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 7)

  • Nkhani: (5 min.) w16.01 13-14 ¶7-10​—Mutu: Kodi Tingasonyeze Bwanji Kuti Timayamikira Chikondi Cha Khristu?​—2Ak 5:14. (th phunziro 8)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 86

  • Khalani Bwenzi la Yehova​—Muzimvetsera Tikakhala Pamisonkhano: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako ngati n’zotheka funsani ana omwe munawasankhiratu mafunso awa: N’chifukwa chiyani tiyenera kumamvetsera tikakhala pamisonkhano? Kodi n’chiyani chingakuthandizeni kuchita zimenezi?

  • Zofunika Pampingo: (10 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 37 mfundo 6 komanso zomwe taphunzira, kubwereza ndi zolinga

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 21 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena