Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 November tsamba 8
  • December 5-11

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 5-11
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 November tsamba 8

December 5-11

2 MAFUMU 13-15

  • Nyimbo Na. 127 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kuchita Zinthu Ndi Mtima Wonse Kumabweretsa Madalitso Ambiri”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mf 13:20, 21​—Kodi chozizwitsa cha pa lembali chimasonyeza kuti kulambira zinthu zakale zopatulika sikulakwa? (w05 8/1 11 ¶3)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mf 13:20–14:7 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 1)

  • Ulendo Wobwereza: (5 min.) Yambitsani phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito phunziro 01 la kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 20)

  • Nkhani: (5 min.) km 8/03 1​—Mutu: Ntchito Imene Imatsitsimula. (th phunziro 11)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 30

  • “Yehova Sangaiwale Khama Limene Tinachita Pomutumikira”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Yehova Saiwala.

  • Zofunika Pampingo: (5 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 30

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 151 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena