Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsamba 10
  • June 13-19

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • June 13-19
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 May tsamba 10

June 13-19

2 SAMUELI 11-12

  • Nyimbo Na. 121 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Musalole Kuti Zilakolako Zoipa Zizikulamulirani”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Sa 12:13​—Kodi Yehova sanaphe Davide ndi Batiseba pa zifukwa ziti? (it-1 590 ¶1)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Sa 11:1-15 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. M’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo pogwiritsa ntchito kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 11)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. M’patseni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale ndipo yambitsani phunziro la Baibulo mu phunziro 01. (th phunziro 13)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 05 mfundo 5 (th phunziro 15)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 29

  • “Muzidziletsa”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Musawononge Moyo Wanu Chifukwa cha Kusuta.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 08

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 28 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena