Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsamba 4
  • May 16-22

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 16-22
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 May tsamba 4

May 16-22

2 Samueli 1-3

  • Nyimbo Na. 103 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Tikuphunzira Chiyani Kuchokera pa Nyimbo Yotchedwa ‘Uta’?”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Sa 1:26​—N’chifukwa chiyani Davide anatchula Yonatani kuti “m’bale wanga”? (it-1 369 ¶2)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Sa 3:1-16 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 3)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mufotokozereni zokhudza phunziro la Baibulo la ulele, kenako m’patseni khadi lodziwitsa anthu za jw.org. (th phunziro 20)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 04 mfundo 5 komanso Zimene Ena Amanena (th phunziro 19)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 107

  • “Chikondi . . . Sichikondwera ndi Zosalungama”: (7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzikumbukira Zimene Chikondi Chimachita Komanso Zimene Sichichita​—Sichikondwera ndi Zosalungama.

  • “Chikondi . . . Chimayembekezera Zinthu Zonse”: (8 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzikumbukira Zimene Chikondi Chimachita Komanso Zimene Sichichita​—Chimayembekezera Zinthu Zonse.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 04

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 2 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena