Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 March tsamba 6
  • March 28–April 3

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 28–April 3
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 March tsamba 6

March 28–April 3

1 SAMUELI 18-19

  • Nyimbo Na. 36 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Tizidzichepetsa Zinthu Zikatiyendera”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 1Sa 19:23, 24​—Kodi Mfumu Sauli anachita bwanji zinthu “ngati mneneri”? (it-2 695-696)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Sa 18:25–19:7 (th phunziro 11)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • “Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki​—Muzithandiza Ophunzira Baibulo Kuti Asiye Makhalidwe Oipa”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzithandiza Amene Mukuphunzira Nawo Baibulo Kuti Asiye Makhalidwe Oipa.

  • Nkhani: (5 min.) km 1/03 1​—Mutu: Ntchito Imene Imafunika Kudzichepetsa. (th phunziro 13)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 31

  • Zofunika Pampingo: (15 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 14 ndime 1-9

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 21 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena