Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 November tsamba 14
  • December 27, 2021–January 2, 2022

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 27, 2021–January 2, 2022
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 November tsamba 14

December 27, 2021–January 2, 2022

OWERUZA 13-14

  • Nyimbo Na. 134 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Makolo Angaphunzire Chiyani kwa Manowa ndi Mkazi Wake?”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Owe 14:2, 3​—Kodi mkazi wa Chifilisitiyu anali “woyenera” bwanji kwa Samisoni? (w05 3/15 26 ¶1)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Owe 14:5-20 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • “Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki​—Muzithandiza Ophunzira Anu Kuti Azidzidyetsa Mwauzimu”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzithandiza Amene Mukuphunzira Nawo Baibulo Kuti Azidzidyetsa Mwauzimu.

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lffi phunziro 02 zomwe taphunzira, kubwereza, komanso zolinga (th phunziro 17)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 110

  • Zofunika Pampingo: (15 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 9 ndime 22-26, mfundo za m’Baibulo tsa. 129-131

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 35 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena