Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 November tsamba 13
  • December 20-26

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 20-26
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 November tsamba 13

December 20-26

OWERUZA 10-12

  • Nyimbo Na. 127 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yefita Anali Munthu Wauzimu”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Owe 11:1​—Kodi timadziwa bwanji kuti Yefita sanali mwana wapathengo? (it-2 26)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Owe 10:1-18 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani chitsanzo cha ulendo woyamba pogwiritsa ntchito kapepala kakuti Kodi Baibulo Mumalikhulupirira? (th phunziro 1)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 4)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lffi phunziro 02 mfundo 5 (th phunziro 3)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 138

  • Anadzipereka Kuyambira Ali Wamng’ono: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso otsatirawa: Kodi vidiyoyi yakuphunzitsani chiyani pa nkhani ya kufunika kophunzitsa anthu ena? kufunika kodzipereka kwa Yehova udakali wamng’ono? kufunika kodzipereka kuti gulu la Yehova likugwiritse ntchito?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 9 ndime 9-21

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 122 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena