October 11-17
YOSWA 10-11
Nyimbo Na. 149 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Anamenyera Nkhondo Aisiraeli”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Yos 10:13—N’chifukwa chiyani n’zosafunika kuti tidziwe zomwe zinali “m’buku la Yasari”? (w09 3/15 32 ¶5)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yos 10:1-15 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
“Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki—Muzilola Kuti Atumiki Anzanu Azikuthandizani”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzigwiritsa Ntchito Zomwe Yehova Watipatsa Kuti Muzisangalala ndi Ntchito Yophunzitsa—Abale Athu.
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lffi phunziro 01 mfundo 4 (th phunziro 14)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 6 ndime 1-11
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 8 ndi Pemphero