Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 September tsamba 9
  • October 4-10

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 4-10
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 September tsamba 9

October 4-10

YOSWA 8-9

  • Nyimbo Na. 127 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Zimene Tikuphunzira pa Nkhani ya Agibeoni”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Yos 8:29​—N’chifukwa chiyani mfumu ya ku Ai anaipachika pamtengo? (it-1 1030)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yos 8:28–9:2 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 2)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. M’patseni kapepala koitanira anthu kumisonkhano yathu, ndipo kenako yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani? (th phunziro 11)

  • Nkhani: (5 min.) lfb mutu 31​—Mutu: Kodi Tingaphunzire Chiyani pa Pangano Limene Yoswa Anachita ndi Agibeoni? (th phunziro 13)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 143

  • Muzisonyeza Kuti Ndinu Wodzichepetsa (1Pe 5:5): (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso otsatirawa: Kodi Petulo ndi Yohane anachita chiyani potsatira malangizo a Yesu okhudza Pasika? Kodi Yesu anaphunzitsa chiyani pa nkhani ya kudzichepetsa usiku woti afa mawa lake? Kodi tikudziwa bwanji kuti Petulo ndi Yohane anaphunzirapo kanthu pa zimenezi? Kodi tingasonyeze bwanji kuti ndife odzichepetsa?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 5 ndime 16-23, mfundo za m’Baibulo tsa. 71-74

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 119 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena