September 20-26
YOSWA 3-5
Nyimbo Na. 65 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Amadalitsa Anthu Achikhulupiriro”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Yos 5:14, 15—Kodi timakhulupirira kuti “kalonga wa gulu lankhondo la Yehova” ndi ndani? (w04 12/1 8 ¶7)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yos 3:1-13 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
“Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki—Muzigwiritsa Ntchito Zinthu Zofufuzira”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzigwiritsa Ntchito Zomwe Yehova Watipatsa Kuti Muzisangalala ndi Ntchito Yophunzitsa—Muzigwiritsa Ntchito Zinthu Zofufuzira.
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lffi phunziro 01 mawu oyamba komanso mfundo 1-2 (th phunziro 15)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 5 ndime 1-10, mawu akumapeto 16, 17
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 32 ndi Pemphero