Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 September tsamba 4
  • September 13-19

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • September 13-19
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 September tsamba 4

September 13-19

YOSWA 1-2

  • Nyimbo Na. 97 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Zimene Mungachite Kuti Zinthu Zizikuyenderani Bwino”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Yos 2:4, 5​—N’chifukwa chiyani Rahabi anapusitsa anthu omwe mfumu inawatuma kuti akafufuze azondi? (w04 12/1 8 ¶6)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yos 2:1-16 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ulendo Wobwereza: Baibulo​—Yob 26:7. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza. (th phunziro 11)

  • Ulendo Wobwereza: (5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako m’patseni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale ndipo yambitsani phunziro la Baibulo. (th phunziro 16)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 56

  • “Pitirizani Kuphunzitsa Mphamvu Zanu za Kuzindikira”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti “Khalani ndi Chikumbumtima Chabwino.”

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 4 ndime 18-21, mfundo za m’Baibulo tsa. 56-59

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 124 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena