Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 July tsamba 15
  • August 30–September 5

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • August 30–September 5
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 July tsamba 15

August 30–September 5

DEUTERONOMO 31-32

  • Nyimbo Na. 78 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Zimene Tingaphunzire pa Mafanizo a mu Nyimbo Youziridwa”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • De 31:12—Kodi makolo Achikhristu angagwiritse ntchito bwanji mfundo ya mulembali? (w04 9/15 27 ¶11)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) De 32:36-52 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 3)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Sinthani ulaliki wanu kuti ugwirizane ndi nkhani imene mwininyumba watchula, ndipo werengani lemba logwirizana ndi nkhaniyo. (th phunziro 12)

  • Nkhani: (5 min.) w07 5/15 15-16​—Mutu: Ana Anu Amaona Zimene Mumachita (th phunziro 16)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 25

  • Anthu Amene Akutsogolera Amatipatsa Chitsanzo Chabwino: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti ‘Muzikumbukira Amene Akutsogolera’ (Ahe 13:7). Kenako funsani omvera kuti: Kodi tikuphunzira chiyani pa chitsanzo cha M’bale T.  J. Sullivan? M’bale George Gangas? M’bale Karl Klein? M’bale Daniel Sydlik?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 4 ndime 1-11, bokosi lakuti Muzimvera Malangizo, Mawu Akumapeto 9-12

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 21 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena