Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 July tsamba 14
  • August 23-29

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • August 23-29
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 July tsamba 14

AUGUST 23-29

DEUTERONOMO 29-30

  • Nyimbo Na. 3 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kutumikira Yehova Sikovuta Kwambiri”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • De 29:4—Kodi chitsanzo cha Aisiraeli omwe anali osakhulupirika chimatiphunzitsa chiyani? (it-1 665 ¶3)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) De 29:1-18 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni khadi lodziwitsa anthu za jw.org. (th phunziro 1)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. M’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo, ndipo yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? (th phunziro 6)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lvs 226-227 ¶3-5 (th phunziro 13)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 73

  • “Kukhala Olimba Mtima Sikovuta Kwambiri”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Musamatsanzire Anthu Amantha, Koma Olimba Mtima.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 3 ndime 16-21, Mfundo za M’Baibulo tsa. 41-44, Mawu Akumapeto 8

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 105 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena