Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 July tsamba 4
  • July 12-18

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • July 12-18
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 July tsamba 4

JULY 12-18

DEUTERONOMO 13-15

  • Nyimbo Na. 38 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Chilamulo Chinkasonyeza Bwanji Kuti Yehova Amaganizira Anthu Osauka?”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • De 14:21—Kodi tingaphunzire chiyani pa lamulo loletsa kuwiritsa mwana wa mbuzi mu mkaka wa mayi ake? (w06 4/1 31)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) De 13:1-18 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ulendo Wobwereza: Kuvutika—1Yo 5:19. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza. (th phunziro 6)

  • Ulendo Wobwereza: (5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 11)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 7

  • “Musamade Nkhawa”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Chikondi Chanu Chisathe Ngakhale Kuti . . . Mukuvutika ndi Umphawi—Congo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 1 ndime 13-18, Mfundo za M’Baibulo tsa. 13-15, Mawu Akumapeto 4

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 37 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena