Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 July tsamba 2
  • July 5-11

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • July 5-11
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 July tsamba 2

JULY 5-11

DEUTERONOMO 11-12

  • Nyimbo Na. 40 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Yehova Amafuna Kuti Tizimulambira Bwanji?”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • De 11:29—Kodi n’kutheka kuti lembali linakwaniritsidwa bwanji? (it-1 925-926)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) De 11:1-12 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • “Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki—Muzisonyeza Kuti Mumawaganizira”: (8 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muziwonjezera Luso Lanu Kuti Muzisangalala ndi Ntchito Yophunzitsa—Muzisonyeza Kuti Mumawaganizira.

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Kuvutika—Yak 1:13. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 1)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 103

  • Zofunika Pampingo: (15 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 1 ndime 7-12, Mawu Akumapeto 2, 3

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 108 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena