Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsamba 11
  • April 12-18

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 12-18
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 March tsamba 11

April 12-18

NUMERI 20-21

  • Nyimbo Na. 114 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muziyesetsa Kukhalabe Ofatsa Mukapanikizika”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Nu 20:23-27​—Kodi tikuphunzira chiyani pa zimene Aroni anachita atalakwitsa zinthu komanso mmene Yehova ankamuonera ngakhale kuti analakwitsa zinthu zina? (w14 6/15 26 ¶12)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Nu 20:1-13 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA WALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 12)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 3)

  • Nkhani: (5 min.) g 1/15 9​—Mutu: Kodi Mungatani Kuti Muziugwira Mtima? (th phunziro 16)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 90

  • Muzilankhula Mawu “Olimbikitsa”: (7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: Kodi kulankhula zosalimbikitsa komanso kukonda kudandaula kumakhudza bwanji ena? N’chiyani chinathandiza m’bale wa mu vidiyoyi kuti asinthe?

  • Musamangotengera Zochita za Anzanu: (8 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: Kodi anthu ambiri amakakamizidwa kuti achite zinthu ziti? Kodi palemba la Ekisodo 23:2 pali malangizo otani?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 129 ndi bokosi lakuti “Kukwapula”

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 13 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena