Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 December tsamba 6
  • December 28, 2020–January 3, 2021

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 28, 2020–January 3, 2021
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 December tsamba 6

December 28, 2020–January 3, 2021

LEVITIKO 16-17

  • Nyimbo Na. 41 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Tsiku la Mwambo Wophimba Machimo Limakukhudzani Bwanji?”: (10 min.)

    • Le 16:12​—Mkulu wa ansembe ankaonekera mophiphiritsira pamaso pa Yehova (w19.11 21 ¶4)

    • Le 16:13​—Mkulu wa ansembe ankapereka zofukiza kwa Yehova (w19.11 21 ¶5)

    • Le 16:14, 15​—Kenako mkulu wa ansembe ankapereka nsembe zophimba machimo a ansembe ndi anthu ena (w19.11 21 ¶6)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Le 16:10​—Kodi mbuzi ya Azazeli imaimira nsembe ya Yesu mu njira ziti? (it-1 226 ¶3)

    • Le 17:10, 11​—N’chifukwa chiyani timakana kuikidwa magazi? (w14 11/15 10 ¶10)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Le 16:1-17 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 3)

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako m’patseni chimodzi mwa zinthu zophunzitsira. (th phunziro 4)

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) fg phunziro 1 ¶1-2 (th phunziro 14)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 70

  • “Kodi Mungakonde Kufunsira Sukulu ya Akhristu Olalikira za Ufumu?”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Amishonale Amagwira Ntchito Yokolola.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (Osapitirira 30 min.) jy mutu 114

  • Mawu Omaliza (Osapitirira 3 min.)

  • Nyimbo Na. 26 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena