Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 December tsamba 2
  • December 7-13

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 7-13
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 December tsamba 2

December 7-13

LEVITIKO 10-11

  • Nyimbo Na. 32 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Tizikonda Yehova Kuposa Mmene Timakondera Achibale Athu”: (10 min.)

    • Le 10:1, 2​—Yehova anapha Nadabu ndi Abihu chifukwa chopereka moto wosaloledwa (it-1 1174)

    • Le 10:4, 5​—Mitembo yawo inachotsedwa mumsasawo

    • Le 10:6, 7​—Yehova analamula Aroni ndi ana ake ena kuti asasonyeze chisoni (w11 7/15 31 ¶16)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Le 10:8-11​—Kodi tikuphunzira chiyani pa mavesiwa? (w14 11/15 17 ¶18)

    • Le 11:8​—Kodi Akhristu ayenera kupewa kudya nyama zoletsedwa m’Chilamulo cha Mose? (it-1 111 ¶5)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Le 10:1-15 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso awa: Kodi Tony anayankha bwanji zimene mwininyumba ananena pofuna kuti asakambirane ndi a Mboniwo? Kodi mungakambirane bwanji ndi munthu mfundo za pa Salimo 1:1, 2?

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. M’patseni kapepala komuitanira kumisonkhano yathu, kenako yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani? (th phunziro 20)

  • Nkhani: (Osapitirira 5 min.) w11 2/15 12​—Mutu: Kodi N’chiyani Chinakhazika Mtima Pansi Mose Atakwiyira Eleazara ndi Itamara? (th phunziro 12)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 51

  • “Timasonyeza Chikondi Tikamachita Zinthu Mogwirizana Ndi Chilango Chochokera kwa Yehova”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Pitirizani Kukhala Okhulupirika ndi Mtima Wonse.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (Osapitirira 30 min.) jy mutu 111 ndime 10-21

  • Mawu Omaliza (Osapitirira 3 min.)

  • Nyimbo Na. 150 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena