Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 June tsamba 2
  • June 1-7

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • June 1-7
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 June tsamba 2

June 1-7

GENESIS 44-45

  • Nyimbo Na. 130 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yosefe Anakhululukira Azichimwene Ake”: (10 min.)

    • Gen. 44:1, 2​—Yosefe anayesa azichimwene ake kuti aone ngati anali atasintha (w15 5/1 14-15)

    • Gen. 44:33, 34​—Yuda anapempha Yosefe kuti amasule Benjamini

    • Gen. 45:4, 5​—Yosefe anatsanzira Yehova pa nkhani yokhululuka

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Gen. 44:13​—Kodi kung’amba zovala kunkatanthauza chiyani? (it-2 813)

    • Gen. 45:5-8​—N’chiyani chingatithandize kupirira anthu ena akatichitira zopanda chilungamo? (w04 8/15 15 ¶15)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Gen. 45:1-15 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Nkhani Yophunzitsadi Anthu, kenako kambiranani phunziro 18 m’kabuku ka Kuphunzitsa.

  • Nkhani: (Osapitirira 5 min.) w06 2/1 31​—Mutu: Kodi Yosefe anagwiritsa ntchito kapu yapadera yasiliva poombeza maula, monga mmene lemba la Genesis 44:5, 15 limamvekera? (th phunziro 18)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 58

  • Zofunika Pampingo: (10 min.)

  • Zimene Gulu Lathu Lachita: (5 min.) Onerani vidiyo yakuti Zimene Gulu Lathu Lachita ya June.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 86 ndime 8-17

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 125 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena