Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 March tsamba 2
  • March 2-8

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 2-8
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 March tsamba 2

March 2-8

GENESIS 22-23

  • Nyimbo Na. 89 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mulungu Anayesa Abulahamu”: (10 min.)

    • Ge 22:1, 2​—Mulungu anauza Abulahamu kuti apereke mwana wake Isaki monga nsembe (w12 1/1 23 ¶4-6)

    • Ge 22:9-12​—Yehova analetsa Abulahamu kuti asaphe Isaki

    • Ge 22:15-18​—Yehova analonjeza Abulahamu kuti adzamudalitsa chifukwa anali womvera (w12 10/15 23 ¶6)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Ge 22:5​—N’chifukwa chiyani Abulahamu anatsimikizira antchito ake kuti Isaki abweranso, pomwe ankadziwa kuti akukamupereka nsembe? (w16.02 11 ¶13)

    • Ge 22:12​—Kodi lembali likusonyeza bwanji kuti Yehova amachita kusankha zinthu zoti adziwiretu? (it-1 853 ¶5-6)

    • Kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ge 22:1-18 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kulankhula Motsimikiza, kenako kambiranani phunziro 15 m’kabuku ka Kuphunzitsa.

  • Nkhani: (Osapitirira 5 min.) it-1 604 ¶5​—Kodi zinatheka bwanji kuti Mulungu aziona kuti Abulahamu ndi munthu wolungama Khristu asanapereke moyo wake monga nsembe? (th phunziro 7)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 4

  • Kumvera Kunawateteza: (15 min.) Onerani vidiyo yakuti Msonkhano Wapachaka wa 2017​—Nkhani Komanso Lemba la Chaka cha 2018​—Mbali ina ya vidiyoyi.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 75

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (Osapitirira 3 min.)

  • Nyimbo Na. 111 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena