Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 December tsamba 4
  • December 16-22

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 16-22
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 December tsamba 4

December 16-22

CHIVUMBULUTSO 13-16

  • Nyimbo Na. 55 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Musamaope Zilombo Zoopsa”: (10 min.)

    • Chiv. 13:1, 2​—Njoka inapereka mphamvu kwa chilombo chokhala ndi mitu 7 ndi nyanga 10 (w12 6/15 8 ¶6)

    • Chiv. 13:11, 15​—Chilombo cha nyanga ziwiri chinapereka moyo kwa chifaniziro cha chilombo choyamba chija (re 194 ¶26; 195 ¶30-31)

    • Chiv. 13:16, 17​—Musalole kulandira chidindo cha chilombo (w09 2/15 4 ¶2)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Chiv. 16:13, 14​—Kodi mitundu ya anthu idzasonkhanitsidwa bwanji “kunkhondo ya tsiku lalikulu la Mulungu Wamphamvuyonse”? (w09 2/15 4 ¶5)

    • Chiv. 16:21​—Kodi ndi uthenga uti umene tidzalengeze dziko la Satanali lisanawonongedwe? (w15 7/15 16 ¶9)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Chiv. 16:1-16 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. (th phunziro 2)

  • Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti, Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? kenako kambiranani naye mfundo za m’vidiyoyi. (th phunziro 11)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 21

  • Muzisonyeza Kuti Simuli Mbali ya Dziko: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Zimene Timaganiza Komanso Kuchita Zizisonyeza Kuti Sitili Mbali ya Dziko. Kenako funsani omvera funso lakuti, Kodi mungatani kuti musakhale mbali ya dziko pa nkhani zokhudza maufulu a anthu komanso mmene boma likuyendetsera zinthu? Kenako oneraninso vidiyo yakuti Tisamachite Zinthu Zosonyeza Kuti Tili Mbali ya Dziko Tikakhala Pagulu. Kenako funsani omvera funso lakuti, Kodi mungakonzekere bwanji kuti musagonje ngati mutayesedwa kuti muchite zinthu zosonyeza kuti muli mbali ya dziko?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 64

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 130 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena