Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 October tsamba 2
  • October 7-13

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 7-13
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 October tsamba 2

October 7-13

Yakobo 3-5

  • Nyimbo Na. 50 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzisonyeza Nzeru Yochokera kwa Mulungu”: (10 min.)

    • Yak. 3:17​—Nzeru yochokera kwa Mulungu ndi yoyera komanso yamtendere (cl 221-222 ¶9-10)

    • Yak. 3:17​—Nzeru yochokera kwa Mulungu ndi yololera, yokonzeka kumvera, yodzaza ndi chifundo komanso zipatso zabwino (cl 223-224 ¶12; 224-225 ¶14-15)

    • Yak. 3:17​—Nzeru yochokera kwa Mulungu ndi yopanda tsankho ndiponso yopanda chinyengo (cl 226-227 ¶18-19)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yak. 4:5​—Kodi Yakobo anagwira mawu a lemba liti? (w08 11/15 20 ¶6)

    • Yak. 4:11, 12​—Kodi “wonenera m’bale wake zoipa” amakhala ‘akuweruza lamulo’ m’njira yotani? (w97 11/15 20-21 ¶8)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yak. 3:1-18 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kusinthasintha Mawu, kenako kambiranani phunziro 10 m’kabuku ka Kuphunzitsa.

  • Nkhani: (Osapitirira 5 min.) w10 9/1 23-24​—Mutu: N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuulula Machimo Athu, Nanga Tiyenera Kuwaulula kwa Ndani? (th phunziro 14)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 53

  • Zofunika Pampingo: (15 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 54

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 97 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena