Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 August tsamba 7
  • August 26–September 1

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • August 26–September 1
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 August tsamba 7

August 26–September 1

AHEBERI 4-6

  • Nyimbo Na. 5 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yesetsani Kuti Mulowe Mumpumulo wa Mulungu”: (10 min.)

    • Aheb. 4:1, 4​—Kodi tsiku la mpumulo wa Mulungu n’chiyani? (w11 7/15 24-25 ¶3-5)

    • Aheb. 4:6​—Muzimvera Yehova (w11 7/15 25 ¶6)

    • Aheb. 4:9-11​—Musamangoyendera maganizo anu (w11 7/15 28 ¶16-17)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Aheb. 4:12​—Kodi “mawu a Mulungu” amene akutchulidwa palembali ndi ati? (w16.09 13)

    • Aheb. 6:17, 18​—Kodi “zinthu ziwiri zosasinthika” zimene zatchulidwa palembali ndi ziti? (it-1 1139 ¶2)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Aheb. 5:1-14 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. (th phunziro 6)

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) lvs 228-229 ¶7-8 (th phunziro 12)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 75

  • “Ntchito Zabwino Zimene Yehova Sangaziiwale”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kodi Mungakonde Kutumikira pa Beteli?.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 48

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 118 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena