Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 June tsamba 2
  • June 4-10

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • June 4-10
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 June tsamba 2

June 4-10

MALIKO 15-16

  • Nyimbo Na. 95 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yesu Anakwaniritsa Maulosi”: (10 min.)

    • Maliko 15:3-5​—Pamene ankaimbidwa mlandu, Yesu sanayankhe chilichonse

    • Maliko 15:24, 29, 30​—Anthu anachita maere pazovala zake ndipo ankamunyoza komanso kumuseka (“kugawana malaya ake akunja” “kupukusa mitu yawo” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 15:24, 29, nwtsty)

    • Maliko 15:43, 46​—Anaikidwa m’manda a anthu olemera (“Yosefe” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 15:43, nwtsty)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Maliko 15:25​—N’chifukwa chiyani pali kusiyana pa nkhani ya nthawi yomwe Yesu anapachikidwa? (“cha m’ma 9 koloko m’mawa” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 15:25, nwtsty)

    • Maliko 16:8​—N’chifukwa chiyani mu Uthenga Wabwino wa Maliko, mu Baibulo la Dziko Latsopano lokonzedwanso lachingelezi, mulibe mawu omaliza aatali komanso aafupi? (“anagwidwa ndi mantha” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 16:8, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Maliko 15:1-15

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) jl mutu 2

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 63

  • “Muzitsatira Mapazi a Khristu Mosamala Kwambiri”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Dzina la Yehova Ndi Lofunika Kwambiri.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 19 ¶8-18 komanso tsamba 208

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 140 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena