Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 December tsamba 3
  • December 11-17

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 11-17
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 December tsamba 3

December 11-17

ZEKARIYA 1-8

  • Nyimbo Na. 146 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Gwirani Chovala cha Munthu Amene ndi Myuda”: (10 min.)

    • [Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Zekariya.]

    • Zek. 8:20-22​—Anthu a mitundu yonse masiku ano akufunafuna Yehova (w14 11/15 27 ¶14)

    • Zek. 8:23​—Anthu amene akuyembekezera kudzakhala padziko lapansili amadzipereka ndi mtima wonse kuthandiza Akhristu odzozedwa (w16.01 23 ¶4; w09 2/15 27 ¶14)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Zek. 5:6-11​—Popeza kuipa kuli paliponse m’dzikoli, kodi ifeyo tili ndi udindo wotani? (w17.10 25 ¶18)

    • Zek. 6:1​—Kodi mapiri awiri amkuwa akuimira chiyani? (w17.10 27-28 ¶7-8)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Zek. 8:14-23

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) g17.6 chikuto​—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) g17.6​—Sonyezani mmene mungapangire ulendo wobwereza pogwiritsa ntchito magazini imene munamusiyira pa ulendo woyamba. Kenako muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) fg phunziro 5 ¶1-2.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 96

  • “Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki​—Muzilalikira Munthu Aliyense wa M’gawo Lanu”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yakuti, Kulalikira Mpaka “Kumalekezero a Dziko Lapansi”.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 11 ¶9-21.

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 134 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena