Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 August tsamba 7
  • August 28–September 3

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • August 28–September 3
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 August tsamba 7

August 28–September 3

EZEKIELI 39-41

  • Nyimbo Na. 107 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mmene Masomphenya a Ezekieli Onena za Kachisi Akutikhudzira”: (10 min.)

    • Ezek. 40:2​—Kulambira Yehova n’kokwezeka kwambiri kuposa kulambira kwa mtundu wina uliwonse (w99 3/1 11 ¶16)

    • Ezek. 40:3, 5​—Yehova adzakwaniritsa cholinga chake chokhudza kulambira koyera (w07 8/1 10 ¶2)

    • Ezek. 40:10, 14, 16​—Tiyenera kutsatira mfundo zapamwamba za makhalidwe abwino za Yehova kuti tizimulambira m’njira yovomerezeka (w07 8/1 11 ¶5)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Ezek. 39:7​—N’chifukwa chiyani tinganene kuti anthu akamaimba mlandu Mulungu kuti ndi amene amachititsa zinthu zopanda chilungamo, amakhala akudetsa dzina lake? (w12 9/1 21 ¶2)

    • Ezek. 39:9​—Pambuyo pa nkhondo ya Aramagedo, kodi zida zankhondo zimene mitundu idzasiye zidzagwiritsidwa ntchito yotani? (w89 8/15 14 ¶20)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ezek. 40:32-47

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) fg phunziro 1 ¶1​—Yambani ndi kumufotokozera za vidiyo yakuti Kodi Mungakonde Kumva Uthenga Wabwino? (koma musaonetse vidiyoyi). Kenako perekani kabukuko.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) fg phunziro1 ¶2—Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) fg phunziro 1 ¶3-4

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 145

  • “Kodi Ndingadzachitenso Liti Upainiya Wothandiza?”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yakuti Yehova Amandithandiza Kuchita Zinthu Zambiri.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 6 ¶1-7 komanso tsamba 58-59

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 92 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena