Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 July tsamba 3
  • July 10-16

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • July 10-16
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 July tsamba 3

July 10-16

EZEKIELI 15-17

  • Nyimbo Na. 11 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Mumakwaniritsa Zimene Mwalonjeza?”: (10 min.)

    • Ezek. 17:1-4​—Ababulo anachotsa Mfumu Yehoyakini pampando n’kuikapo Zedekiya (w07 7/1 12 ¶6)

    • Ezek. 17:7, 15​—Zedekiya sanakhulupirike, m’malomwake anapempha thandizo kwa Aiguputo (w07 7/1 12 ¶6)

    • Ezek. 17:18, 19​—Yehova ankafuna kuti Zedekiya akwaniritse zomwe analonjeza (w12 10/15 30 ¶11; w88 9/15 17 ¶8)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Ezek. 16:60​—Kodi “pangano limene lidzakhalepo mpaka kalekale,” ndi chiyani, ndipo ndi ndani ali m’panganoli? (w88 9/15 17 ¶7)

    • Ezek. 17:22, 23​—Kodi ndi ndani amene ali “nsonga yanthete” yomwe Yehova anati adzabzala? (w07 7/1 12 ¶6)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ezek. 16:28-42

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) wp17.4 chikuto​—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) wp17.4 chikuto​—Mufotokozereni za vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? (Koma musaonetse vidiyoyi).

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) fg phunziro 11 ¶1-2​—Muitanireni kumisonkhano.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 36

  • Muzikwaniritsa Zimene Munalonjeza pa Tsiku la Ukwati Wanu Ngakhale Pamene Banja Lanu Silikuyenda Bwino: (10 min.) Nkhani yokambidwa ndi mkulu yochokera mu Galamukani! ya March 2014, tsamba 14-15.

  • Khalani Bwenzi la Yehova​—Uzinena Zoona: (5 min.) Onetsani Vidiyo yakuti Khalani Bwenzi la Yehova​—Uzinena Zoona. Kenako itanani ana amene munawasankhiratu kuti abwere kutsogolo ndipo afunseni mafunso okhudza vidiyoyi.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 3 ¶13-22, komanso tsamba 36-37, 38

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 137 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena