Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 June tsamba 4
  • June 12-18

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • June 12-18
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 June tsamba 4

June 12-18

MALIRO 1-5

  • Nyimbo Na. 128 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mtima Wodikira Umatithandiza Kuti Tipirire”: (10 min.)

    • [Onetsani vidiyo yakuti, Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Maliro.]

    • Maliro 3:20, 21, 24​—Yeremiya anasonyeza kuti anali ndi mtima wodikira ndipo ankadalira Yehova (w12 6/1 14 ¶3-4; w11 9/15 8 ¶8)

    • Maliro 3:26, 27​—Kupirira mayesero kudzatithandiza kuthana ndi mavuto amene tingakumane nawo m’tsogolo (w07 6/1 11 ¶3-4)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Maliro 2:17​—Kodi ndi mawu ati kwenikweni amene Yehova “ananena” okhudza Yerusalemu? (w07 6/1 9 ¶2)

    • Maliro 5:7​—Kodi Yehova amaimba anthu mlandu chifukwa cha zolakwa za makolo awo akale? (w07 6/1 10 ¶5)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Maliro 2:20–3:12

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) g17.3 chikuto​—Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) g17.3 chikuto​—Muitanireni kumisonkhano yathu.

  • Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w11 9/15 9-10 ¶11-13​—Mutu: Yehova Ndi Cholowa Changa.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 126

  • Zofunika Pampingo: (8 min.) Mukhoza kukambirana “Kalata Yochokera ku Bungwe Lolamulira” ya mu Buku Lapachaka. (yb 17 2-5)

  • Zimene Gulu Lathu Lachita: (7 min.) Onetsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Lathu Lachita ya June 2017.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 2 ¶13-22

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 100 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena