Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 July tsamba 4
  • July 11-17

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • July 11-17
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 July tsamba 4

July 11-17

MASALIMO 69-73

  • Nyimbo Na. 92 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Anthu a Mulungu ndi Odzipereka Potumikira Yehova”: (10 min.)

    • Sal. 69:9​—Tiyenera kumachita zinthu zosonyeza kuti ndife odzipereka kwa Mulungu (w10 12/15 7-11 ndime 2-17)

    • Sal. 71:17, 18​—Akhristu achikulire angathandize achinyamata kukhala odzipereka (w14 1/15 23-25 ndime 4-10)

    • Sal. 72:3, 12, 14, 16-19​—Tikakhala odzipereka timafunitsitsa kuuza ena zimene Ufumu wa Mulungu udzatichitire (w15 10/1 16 ndime 3; w10 8/15 32 ndime 19-20)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Sal. 69:4, 21​—Kodi mavesi amenewa akukwaniritsa bwanji ulosi wonena za Mesiya? (w11 8/15 11 ndime 17; w11 8/15 15 ndime 15)

    • Sal. 73:24​—Kodi Yehova amatsogolera bwanji atumiki ake ku ulemerero? (w13 2/15 25-26 ndime 3-4)

    • Kodi ndaphunzira chiyani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 73:1-28

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) wp16.4 tsamba loyamba​—Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) wp16.4 tsamba loyamba

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) fg phunziro 5 ndime 3 ndi 4

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 140

  • “Kodi Mungachite Upainiya kwa Chaka Chimodzi?”: (15 min.) Kambiranani mwachidule nkhaniyi komanso “Ndandanda ya Upainiya Wokhazikika.” Kenako onerani vidiyo ya pa JW Broadcasting ya mutu wakuti, Kusankha Ntchito Imene Sidzatha Mpaka Kalekale. (Pitani pamene alemba kuti MAVIDIYO ENA > ACHINYAMATA.) Mukamaliza kuonera vidiyoyi, kambiranani zimene tikuphunzirapo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 2 ndime 1-12.

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 123 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena