Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 June tsamba 4
  • June 13-19

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • June 13-19
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 June tsamba 4

June 13-19

MASALIMO 38-44

  • Nyimbo Na. 4 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Amasamalira Anthu Omwe Akudwala”: (10 min.)

    • Sal. 41:1, 2—Wodala ndi munthu amene amaganizira anthu onyozeka (w15 12/15 24 ndime 7; w91 10/1 14 ndime 6)

    • Sal. 41:3—Yehova amasamalira owongoka mtima pamene akudwala (w08 9/15 5 ndime 12-13)

    • Sal. 41:12—Kudziwa kuti matenda adzatha kungathandize anthu omwe akudwala kuti apirire (w15 12/15 27 ndime 18-19; w08 12/15 6 ndime 15)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Sal. 39:1, 2—Kodi n’chiyani chingatithandize kuti tizikhala osamala poyankhula? (w09 5/15 4 ndime 6; w06 5/15 20 ndime 11)

    • Sal. 41:9—Kodi Yesu anasonyeza bwanji kuti zimene zinachitikira Davide zidzachitikiranso iyeyo? (w11 8/15 13 ndime 5; w08 9/15 5 ndime 11)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 42:6–43:5

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Tsamba loyamba la g16.3

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Tsamba loyamba la g16.3

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) fg phunziro 2 ndime 4-5—Pomaliza fotokozerani munthuyo zokhudza vidiyo yakuti Kodi Mulungu Ali ndi Dzina?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 128

  • Yang’ananibe Pamphoto!: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo ya pa jw.org yakuti Khalani Bwenzi la Yehova—Yang’ananibe Pamphoto (Nyimbo Na. 24). (Pitani pamene palembedwa kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA.) Kenako kambiranani mbali yakuti “Kuyerekezera: Moyo Wapanopa ndi Wam’tsogolo,” pogwiritsa ntchito mafunso otsatirawa: Kodi ndi zinthu ziti zomwe zidzasinthe m’Paradaiso? Kodi ndi zinthu zabwino ziti zimene mukuyembekezera? Kodi kuganizira zimene mukuyembekezera m’tsogolo kungakuthandizeni bwanji kuti mupirire?—2 Akor. 4:18.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) cl mutu 31 ndime 21-23, ndi bokosi patsamba 319

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 36 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena