Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 May tsamba 4
  • May 9-15

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 9-15
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 May tsamba 4

May 9-15

MASALIMO 1-10

  • Nyimbo 99 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Tizilemekeza Yesu Kuti Tikhale Pamtendere ndi Yehova”: (10 min.)

    • [Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Masalimo.]

    • Sal. 2:1-3—Baibulo linaneneratu kuti anthu adzakana kukhulupirira Yehova ndi Yesu (w04 7/15 15-17 ndime 4-8; it-1-E 507; it-2-E 386 ndime 3)

    • Sal. 2:8-12—Anthu amene amalemekeza Mfumu yosankhidwa ndi Yehova adzapeza moyo (w04 8/1 5 ndime 2-3)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Sal. 2:7—Kodi “lamulo la Yehova” n’chiyani? (w06 5/15 17 ndime 6)

    • Sal. 4:4—Kodi mawu akuti “Lankhulani mumtima mwanu, muli pabedi panu, ndipo mukhale chete” amatanthauza chiyani? (w11 5/15 31 ndime 18)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Salimo 8:1–9:10

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) wp16.3 Nkhani ya pachikuto—Werengani lemba pogwiritsa ntchito foni kapena chipangizo china chamakono.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) wp16.3 Nkhani ya pachikuto—Chitani chitsanzo chosonyeza mwininyumba akukana kumuwerengera lemba mu Baibulo la Dziko Latsopano. Kenako gwiritsani ntchito Laibulale ya JW kuti mumusonyeze mmene lembalo analimasulira mu Mabaibulo ena.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bh 12 ndime 12-13—Limbikitsani wophunzirayo kuti apange dawunilodi Laibulale ya JW mufoni yake.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 138

  • Uzilemekeza Nyumba ya Yehova: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo ya pa jw.org yakuti Khalani Bwenzi la Yehova—Uzilemekeza Nyumba ya Yehova (Pitani pamene palembedwa kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA.) Kenako itanani ana ang’onoang’ono kuti abwere kupulatifomu ndipo muwafunse zomwe aphunzira mu vidiyoyo.

  • Dzina la Mulungu M’Malemba Achiheberi: (10 min.) Nkhani yochokera mu Kabuku Kothandiza Kuphunzira Baibulo mutu 1.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) cl mutu 30 ndime 1-9

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 11 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena