Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 April tsamba 2
  • April 4-10

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 4-10
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 April tsamba 2

April 4-10

YOBU 16-20

  • Nyimbo Na. 79 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Tizilimbikitsa Anzathu Powayankhula Mokoma Mtima”: (10 min.)

    • Yobu 16:4, 5—Munthu wopereka malangizo ayenera kuyankhula molimbikitsa kwa ena (w90 3/15 27 ndime 1-2)

    • Yobu 19:2—Yobu analira chifukwa cha mawu opweteka a Bilidadi (w06 3/15 15 ndime 5; w94 10/1 32)

    • Yobu 19:25—Chiyembekezo chakuti akufa adzauka chinathandiza Yobu pa nthawi yomwe anakumana ndi mayesero aakulu (w06 3/15 15 ndime 4; it-2-E 735 ndime 2-3)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yobu 19:20 [Mawu am’munsi]—Kodi Yobu ankatanthauza chiyani pamene ananena kuti, “Ndapulumuka ndi khungu la mano anga”? (w06 3/15 14 ndime 13; it-2-E 977 ndime 1)

    • Yobu 19:26—Popeza kuti munthu sangathe kuona Yehova, kodi Yobu ankatanthauza chiyani ponena kuti “ndidzaona Mulungu”? (w94 11/15 19 ndime 17)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: Yobu 19:1-23 (Osapitirira 4 min.)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kukonzekera Ulaliki wa Mwezi Uno: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani mavidiyo a zitsanzo za ulaliki ndipo kenako kambiranani mfundo zikuluzikulu za m’mavidiyowo. Limbikitsani ofalitsa kuti akonze ulaliki wawowawo.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 42

  • “Nkhani Zatsopano Zothandiza Poyamba Kukambirana ndi Anthu”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Limbikitsani onse kuti azigwiritsa ntchito nkhani zakuti, “Kodi Baibulo Limanena Zotani?” pofuna kuyambitsa maphunziro a Baibulo.

  • Mafunso Ochokera kwa Owerenga: (5 min.) Nkhani yokambidwa ndi mkulu, kuchokera mu Nsanja ya Olonda ya February 15, 2015, tsamba 30, ndime 4-6.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: cl mutu 28 ndime 10-17 (30 min.)

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 65 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena