Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 January tsamba 6
  • January 25-31

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • January 25-31
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 January tsamba 6

January 25-31

EZARA 6-10

  • Nyimbo Na. 10 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Amafuna Kuti Tizimutumikira ndi Mtima Wonse”: (10 min.)

    • Ezara 7:10—Ezara anakonzekeretsa mtima wake

    • Ezara 7:12-28—Ezara anakonzekera kubwerera ku Yerusalemu

    • Ezara 8:21-23—Ezara ankakhulupirira kuti Yehova ateteza atumiki ake

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Ezara 9:1, 2—N’chifukwa chiyani kukwatirana ndi anthu a mitundu ina kunali koopsa? (w06 1/15 20 ndime 1)

    • Ezara 10:3—N’chifukwa chiyani ana anachotsedwa pamodzi ndi akazi? (w06 1/15 20 ndime 2)

    • Kodi ndaphunzira chiyani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: Ezara 7:18-28 (Osapitirira 4 min.)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gawirani kabuku kakuti Uthenga Wabwino, kenako kambiranani phunziro 8, funso 1 ndime 1. Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Chitani chitsanzo chosonyeza ulendo wobwereza kwa munthu amene analandira kabuku kakuti Uthenga Wabwino. Mukambirane naye phunziro 8, funso 1 ndime 2. Mumuuze nkhani imene mudzaphunzire ulendo wotsatira.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) Chitani chitsanzo cha munthu akuchititsa phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito kabuku kakuti Uthenga Wabwino phunziro 8, funso 2.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 138

  • “Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki: Muzisiya Mafunso Oti Mudzakambirane Ulendo Wotsatira”: (7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya mutu wakuti Luso Loti Tiwonjezere mu January. Vidiyoyi ikusonyeza ofalitsa akufunsa mwininyumba funso lomwe lingamuthandize kuti adzachite ulendo wobwereza atagawira magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! a mwezi wa January komanso kabuku ka Uthenga Wabwino.

  • Zofunika pampingo: (8 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: cl mutu 25 ndime 1-8, (30 min.)

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu wa Mawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 120 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena