Zilengezo
◼ Mabuku ogawira mu April: Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! May ndi June: Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? kapena kapepala kakuti, Kodi Mukufuna Kudziwa Choonadi? July: Kabuku kakuti, Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu, Mverani Mulungu ndi kakuti, Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha.