Zilengezo
◼ Mabuku ogawira January ndi February: Kabuku kakuti, Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu. March ndi April: Nsanja ya Olonda ndi Galamukani!
◼ Kuyambira mwezi wa February 2015, oyang’anira dera adzayamba kukamba nkhani ya onse ya mutu wakuti “Zochitika za Padzikoli Zikusintha.”